Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anatenga ndende ena a abale ao zikwi mazana awiri, akazi, ana amuna ndi akazi, nalandanso kwa iwo zofunkha zambiri, nabwera nazo zofunkhazo ku Samariya,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:8 nkhani