Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 28:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nafukizanso yekha m'cigwa ca mwana wa Hinomu, napsereza ana ace m'moto, monga mwa zonyansa za amitundu, amene Yehova anawainga pamaso pa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:3 nkhani