Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 28:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahazi anasonkhanitsa zipangizo za m'nyumba ya Mulungu, naduladula zipangizo za m'nyumba ya Mulungu, natseka pa makomo a nyumba ya Yehova, nadzimangira maguwa a nsembe m'ngondya ziri zonse za Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:24 nkhani