Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 26:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Uziya anapsa mtima, mbale ya zofukiza iri m'dzanja lace kufukiza nayo; ndipo pakupsa mtima nao ansembe, khate linabuka pamphumi pace, pamaso pa ansembe m'nyumba ya Yehova, pambali pa guwa lofukizapo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:19 nkhani