Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 26:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

natsutsana ndi mfumu Uziya, nati kwa iye, Sikuyenera inu, Uziya, kufukizira Yehova, koma ansembe, ana a Aroni opatulidwira kufukiza; turukani m'malo opatulika; pakuti mwalakwa; Yehova Mulungu sakulemekezanipo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:18 nkhani