Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amaziya anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai; ndi dzina la mace ndiye Yehoadana wa ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:1 nkhani