Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 24:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ataitsiriza, anabwera nazo ndalama zotsala kwa mfumu ndi Yehoyada, napanga nazo zipangizo za nyumba ya Yehova, zipangizo za kutumikira nazo, ndi kupereka nsembe nazo, ndi zipande, ndi zipangizo za golidi ndi siliva. Ndipo anapereka kosalekeza nsembe zopsereza m'nyumba ya Yehova masiku onse a Yehoyada.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24

Onani 2 Mbiri 24:14 nkhani