Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 23:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Alevi amzinge mfumu pozungulirapo, yense ndi zida zace m'dzanja mwace; ndipo ali yense wolowa m'nyumba aphedwe; nimukhale inu pamodzi ndi mfumu pakulowa ndi pakuturuka iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:7 nkhani