Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 22:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehosafati mwana wamkazi wa mfumu anatenga Yoasi mwana wa Ahaziya, namuba pakati pa ana a mfumu ophedwa, namlonga iye ndi mlezi wace m'cipinda cogonamo. Momwemo Yehosafati mwana wamkazi wa mfumu Yehoramu, mkazi wa Yehoyada wansembe (popeza ndiye mlongo wace wa Ahaziya), anambisira Ataliya, angamuphe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 22

Onani 2 Mbiri 22:11 nkhani