Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 22:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo okhala m'Yerusalemu anamlonga Ahaziya mwana wace wamng'ono akhale mfumu m'malo mwace; pakuti gulu la anthu, adadzawo pamodzi ndi Aarabu kucigono, adapha ana oyamba onse. Momwemo Ahaziya mwana wa Yehosafati anakhala mfumu ya Yuda.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 22

Onani 2 Mbiri 22:1 nkhani