Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 21:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anali nao abale ace, ana a Yehosafati, Azariya, ndi Yehieli, ndi Zekariya, ndi Azariya, ndi Mikaeli, ndi Sefatiya, onsewa ndiwe ana a Yehosafati mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 21

Onani 2 Mbiri 21:2 nkhani