Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, nditi ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba, kumpatulira iyo, ndi kufukiza pamaso pace zonunkhira za pfungo lokoma, ndiyo ya mkate woonekera wacikhalire, ndi ya nsembe zopsereza, m'mawa ndi madzulo, pamasabata, ndi pokhala mwezi, ndi pa madyerero oikika a Yehova Mulungu wathu. Ndiwo macitidwe osatha m'Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 2

Onani 2 Mbiri 2:4 nkhani