Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Huramu anatinso, Alemekezedwe Yehova Mulungu wa Israyeli, amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi, nampatsa mfumu Davide mwana waluso, wodziwa nzeru ndi waluntha, ammangire Yehova nyumba, ndiponso nyumba ya ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 2

Onani 2 Mbiri 2:12 nkhani