Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 19:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehosafati anaikanso m'Yerusalemu Alevi, ndi ansembe ena, ndi akuru a nyumba za makolo m'Israyeli, aweruzire Yehova, nanene mirandu. Ndipo anabwerera kudza ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 19

Onani 2 Mbiri 19:8 nkhani