Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Asa anali nao ankhondo ogwira zikopa ndi mikondo, a m'Yuda zikwi mazana atatu; ndi a m'Benjamini ogwira malihawo ndi okoka mauta zikwi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu; onsewo ngwazi zamphamvu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:8 nkhani