Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Abiya anagona ndi makolo ace, ndipo anamuika m'mudzi wa Davide; ndi Asa mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace, m'masiku ace dziko linaona bata zaka khumi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:1 nkhani