Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Semaya mneneri anadza kwa Rehabiamu, ndi kwa akalonga a Yuda, atasonkhana ku Yerusalemu cifukwa ca Sisaki, nati nao, Atero Yehova, Inu mwandisiya Ine, cifukwa cace Inenso ndasiya inu m'dzanja la Sisaki.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 12

Onani 2 Mbiri 12:5 nkhani