Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 11:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuwatsata iwo anadza ku Yerusalemu, ocokera m'mafuko onse a Israyeli, iwo akupereka mitima yao kufuna Yehova Mulungu wa Israyeli, kudzaphera Yehova Mulungu wa makolo ao nsembe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 11

Onani 2 Mbiri 11:16 nkhani