Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 10:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuona Aisrayeli onse kuti mfumu sinawamvera anthuwo, anamyankha mfumu, ndi kuti, Tiri naye ciani Davide? inde tiribe colowa m'mwana wa Jese; tiyeni kwathu, Aisrayeli inu; yang'anira nyumba yako tsopano, Davide. Momwemo Aisrayeli onse anamuka ku mahema ao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 10

Onani 2 Mbiri 10:16 nkhani