Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nutenge nsupa ya mafutayo, nuwatsanulire pamutu pace, nunene, Atero Yehova; Ndakudzoza iwe ukhale mfumu pa Israyeli. Utatero, tsegula pakhomo, nuthawe osacedwa,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:3 nkhani