Niti mfumu kwa Hazaeli, Tenga caufulu m'dzanja lako, nukamkumike munthu wa Mulungu, nukafunsire Yehova mwa iye, ndi kuti, Ndidzacira kodi nthenda iyi?