Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 5:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Gehazi anatsata Namani. Ndipo pamene Namani anaona wina alikumthamangira, anatsika pagareta kukomana naye, nati, Nkwabwino kodi?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:21 nkhani