Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Gehazi, mnyamata wa Elisa, munthu wa Mulungu, anati, Taona, mbuye wanga analekera Namani uyu wa ku Aramu osalandira m'manja ace cimene anabwera naco; pali Yehova, ndidzathamangira ndi kulandira kanthu kwa iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:20 nkhani