Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo anati kwa mwamuna wace, Taona, tsopano ndidziwa kuti munthu uyu wakupitira pathu pano cipitire ndiye munthu woyera wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:9 nkhani