Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa anabwera ku Giligala, koma m'dzikomo munali njala; ndi ana a aneneri anali kukhala pansi pamaso pace; ndipo anati kwa mnyamata wace, Ika nkhali yaikuruyo, uphikire ana a aneneri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:38 nkhani