Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wina wa akazi a ana a aneneri anapfuula kwa Elisa, ndi kuti, Mnyamata wanu, mwamuna wanga wafa; mudziwa kuti mnyamata wanu anaopa Yehova; ndipo wafika wamangawa kunditengera ana anga awiri akhale akapolo ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:1 nkhani