Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mesa mfumu ya Moabu anali mwini nkhosa, akapereka kwa mfumu ya Israyeli ubweya wa ana a nkhosa zikwi zana limodzi, ndi wa mphongo zikwi zana limodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:4 nkhani