Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehoramu mwana wa Ahabu analowa ufumu wa Israyeli m'Samariya m'caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yehosafati mfumu ya Yuda, nakhala mfumu zaka khumi ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:1 nkhani