Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 25:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anamva akazembe onse a makamu, iwo ndi anthu ao, kuti mfumu ya Babulo adaika Gedaliya wowalamulira, anadza kwa Gedaliya ku Mizipa, ndiwo Ismayeli mwana wa Netaniya, ndi Yohanana mwana wa Kareya, ndi Seraya mwana wa Tanumeti wa ku Netofa, ndi Yazaniya mwana wa Mmakati, iwo ndi anthu ao omwe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:23 nkhani