Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 25:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Msinkhu wace wa nsanamira imodzi ndiwo mikono khumi mphambu isanu ndi itatu, ndi pamwamba pace mutu wamkuwa; ndi msinkhu wace wa mutuwo ndiwo mikono itatu, ndi ukonde, ndi makangaza pamutu pouzinga, zonse zamkuwa; ndi nsanamira inzace inali nazo zomwezo pamodzi ndi ukonde.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:17 nkhani