Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 24:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacoka naye Yoyakini kumka naye ku Babulo, ndi mace wa mfumu, ndi akazi a mfumu, ndi adindo ace, ndi omveka a m'dziko; anacoka nao andende ku Yerusalemu kumka nao ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:15 nkhani