Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 24:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nacoka nao a m'Yerusalemu onse, ndi akalonga onse, ndi ngwazi zonse, ndiwo andende zikwi khumi, ndi amisiri onse, ndi osula onse; sanatsala ndi mmodzi yense, koma anthu osauka okha okha a m'dziko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:14 nkhani