Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoyakimu anapereka siliva ndi golidi kwa Farao, koma anasonkhetsa dzikoli lipereke ndalamazi; monga mwa lamulo la Farao anasonkhetsa anthu a m'dziko siliva ndi golidi, yense monga mwa kuyesedwa kwace, kuzipereka kwa Farao-Neko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:35 nkhani