Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao-Neko analonga ufumu Eliyakimu mwana wa Yosiya, m'malo mwa Yosiya atate wace, nasanduliza dzina lace likhale Yoyakimu; koma anapita naye Yoahazi, nafika iye m'Aigupto, nafa komweko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:34 nkhani