Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 22:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, taona, ndidzakusonkhanitsa ukhale ndi makolo ako, nudzatengedwa ulowe m'manda mwako mumtendere; ndipo sudzaona m'maso mwako coipa conse ndidzacifikitsira malo ano. Ndipo anambwezera mfumu mau.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22

Onani 2 Mafumu 22:20 nkhani