Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaceuka, nawaona, nawatemberera m'dzina la Yehova. Ndipo kuthengo kunaturuka zimbalangondo ziwiri zazikazi, ndi kupwetedza mwa iwo ana makumi anai mphambu awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:24 nkhani