Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacokako kukwera ku Beteli, ndipo iye ali cikwerere m'njiramo, munaturuka anyamata ang'ono m'mudzimo, namseka, nati kwa iye, Takwera wadazi, takwera wadazi!

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:23 nkhani