Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 19:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace okhalamo ao anali ofok a manja, anaopsedwa, nacita manyazi, ananga udzu wa kuthengo, ndi msipu wauwisi, ndi udzu wa patsindwi, ndi tirigu wopserera asanakule.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:26 nkhani