Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mpaka ndifika ndi kumuka nanu ku dziko lakunga dziko lanu, dziko la tirigu ndi vinyo, dziko la mkate ndi minda yampesa, dziko la azitona ndi la uci; kuti mukhale ndi moyo osafai; nimusamvere Hezekiya akakukopani, ndi kuti, Yehova adzatilanditsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:32 nkhani