Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamvere Hezekiya; pakuti Itero mfumu ya Asuri, Mupangane nane zamtendere, nimuturukire kwa ine, ndi kumadya yense ku mpesa wace, ndi yense ku mkuyu wace, ndi kumwa yense madzi a m'citsime cace;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:31 nkhani