Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Eliyakimu mwana wa Hilikiya, ndi Sebina, ndi Yoa, anati kwa kazembeyo, Mulankhule ndi anyamata anu m'Ciaramu; popeza ticimva ici; musalankhule nafe m'Ciyuda, comveka ndi anthu okhala palinga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:26 nkhani