Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa sanamvera mau a Yehova Mulungu wao, koma analakwira cipangano cace, ndico zonse anazilamulira Mose mtumiki wa Yehova; sanazimvera kapena kuzicita.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:12 nkhani