Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma Yehova amene anakukwezani kukuturutsani m'dziko la Aigupto ndi mphamvu yaikuru, ndi dzanja lotambasuka, Iyeyu muzimuopa, ndi Iyeyu muzimgwadira, ndi Iyeyu muzimphera nsembe;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:36 nkhani