Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero ananena ndi mfumu ya Asuri, kuti, Amitundu aja mudawacotsa kwao, ndi kuwakhalitsa m'midzi ya Samariya, sadziwa makhalidwe a Mulungu wa dzikoli; cifukwa cace anawatumizira mikango pakati pao, ndipo taonani, irikuwapha; popeza sadziwa makhalidwe a Mulungu wa dzikoli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:26 nkhani