Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahazi anatuma mithenga kwa Tigilati Pilesere mfumu ya Asuri, ndi kuti, Ine ndine kapolo wanu ndi mwana wanu; kwerani, mudzandipulumutse m'dzanja la mfumu ya Aramu, ndi m'dzanja la mfumu ya Israyeli anandiukirawo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:7 nkhani