Ndipo Uriya wansembe anamanga guwa la nsembelo, monga mwa zonse anazitumiza mfumu Ahazi zocokera ku Damasiko; momwemo Uriya wansembe analimanga asanabwere mfumu ku Damasiko.