Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 15:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagona Yotamu ndi makolo ace, namuika pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide kholo lace; nakhala mfumu m'malo mwace Ahazi mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15

Onani 2 Mafumu 15:38 nkhani