Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 15:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku a Peka mfumu ya Israyeli anadza Tigilati Pilesere mfumu ya Asuri, nalanda Ijoni, ndi Abeli-BeteMaaka, ndi Yanoa, ndi Kedesi, ndi Hazori, ndi Gileadi, ndi Galileya, dziko lonse la Nafitali; nawatenga andende kumka nao ku Asuri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15

Onani 2 Mafumu 15:29 nkhani