Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 14:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anabweza malire a Israyeli kuyambira polowera ku Hamati mpaka nyanja ya kucidikha, monga mwa mau a Yehova Mulungu wa Israyeli, amene ananena ndi dzanja la mtumiki wace Yona mwana wa Amitai mneneriyo, ndiye wa Gati-heferi,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:25 nkhani