Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 12:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yozakara mwana wa Simeati, ndi Yosabadi mwana wa Someri, anyamata ace, anamkantha, nafa iye; ndipo anamuika kwa makolo ace m'mudzi wa Davide; ndi Amaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:21 nkhani